Yohane 9:9 - Buku Lopatulika9 Ena ananena, kuti, Ndiyeyu; ena ananena, Iai, koma afanana naye. Iyeyu anati, Ndine amene. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ena ananena, kuti, Ndiyeyu; ena ananena, Iai, koma afanana naye. Iyeyu anati, Ndine amene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ena adati, “Ndiye amene.” Ena nkumati, “Iyai, akungofanafana naye.” Koma mwiniwakeyo adati, “Ai ndithu, ndine amene.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ena ananena kuti anali yemweyo. Ena anati, “Ayi, sakuoneka ngati yemweyo.” Koma iye mwini ananenetsa kuti, “Munthuyo ndine.” Onani mutuwo |