Yohane 9:8 - Buku Lopatulika8 Chifukwa chake anzake ndi iwo adamuona kale, kuti anali wopemphapempha, ananena, Kodi si uyu uja wokhala ndi kupemphapempha? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chifukwa chake anzake ndi iwo adamuona kale, kuti anali wopemphapempha, ananena, Kodi si uyu uja wokhala ndi kupemphapempha? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamenepo anzake ndi anthu amene kale ankamuwona akupemphapempha adati, “Kodi uyu si uja ankakhala pansi apa nkumangopempha?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Anzake ndi iwo amene anamuona iye poyamba akupempha anafunsa kuti, “Kodi uyu si munthu amene amapemphapempha uja?” Onani mutuwo |