Yohane 9:30 - Buku Lopatulika30 Munthuyu anayankha nati kwa iwo, Pakuti chozizwa chili m'menemo, kuti inu simudziwa kumene achokera, ndipo ananditsegulira maso anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Munthuyu anayankha nati kwa iwo, Pakuti chozizwa chili m'menemo, kuti inu simudziwa kumene achokera, ndipo ananditsegulira maso anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Munthuyo adati, “Pakudabwitsatu mpamenepa: kuti inuyo simukudziŵa kumene Iye wachokera, komabe wandipenyetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Munthuyo anayankha kuti, “Tsopano izi ndi zodabwitsa! Inu simukudziwa kumene akuchokera, komabe iye watsekula maso anga. Onani mutuwo |