Yohane 9:27 - Buku Lopatulika27 Iye anayankha iwo, Ndinakuuzani kale, ndipo simunamve; mufuna kumvanso bwanji? Kodi inunso mufuna kukhala ophunzira ake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Iye anayankha iwo, Ndinakuuzani kale, ndipo simunamva; mufuna kumvanso bwanji? Kodi inunso mufuna kukhala ophunzira ake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Iye adati, “Ndakuuzani kale, koma simumasamalako. Nanga chifukwa chiyani mukufuna kuzimvanso? Kapenatu nanunso mukufuna kukhala ophunzira ake eti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Iye anayankha kuti, “Ine ndakuwuzani kale ndipo inu simunamvetsetse. Chifukwa chiyani mukufuna mumvenso? Mukufuna kuti inu mukhale ophunzira akenso?” Onani mutuwo |