Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 9:26 - Buku Lopatulika

26 Chifukwa chake anati kwa iye, Anakuchitira iwe chiyani? Anakutsegulira iwe maso bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Chifukwa chake anati kwa iye, Anakuchitira iwe chiyani? Anakutsegulira iwe maso bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Iwo adamufunsa kuti, “Kodi anachita chiyani pamene anakupenyetsa?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Kenaka anamufunsa kuti, “Kodi Iye anachita chiyani kwa iwe? Iye anatsekula motani maso ako?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 9:26
7 Mawu Ofanana  

Yankha chitsiru monga mwa utsiru wake, kuti asadziyese wanzeru.


Ndipo anamfunsa Baruki, kuti, Utifotokozeretu, Unalemba bwanji mau awa onse ponena iye?


Ndipo alembi ndi Afarisi analikumzonda Iye, ngati adzachiritsa tsiku la Sabata; kuti akapeze chomneneza Iye.


Pamenepo anenana ndi iye, Nanga maso ako anatseguka bwanji?


Pamenepo ndipo Afarisi anamfunsanso, umo anapenyera. Ndipo anati kwa iwo, Anapaka thope m'maso mwanga, ndinasamba, ndipo ndipenya.


Pamenepo iyeyu anayankha, Ngati ali wochimwa, sindidziwa; chinthu chimodzi ndichidziwa, pokhala ndinali wosaona, tsopano ndipenya.


Iye anayankha iwo, Ndinakuuzani kale, ndipo simunamve; mufuna kumvanso bwanji? Kodi inunso mufuna kukhala ophunzira ake?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa