Yohane 9:23 - Buku Lopatulika23 Chifukwa cha ichi atate wake ndi amake anati, Ali wamsinkhu; mumfunse iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Chifukwa cha ichi atate wake ndi amake anati, Ali wamsinkhu; mumfunse iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Nchifukwa chake makolo akewo adati, “Ngwamkulu, mufunseni mwiniwakeyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ichi ndi chifukwa chake makolo ake anati, “Mufunseni iye ndi wamkulu.” Onani mutuwo |