Yohane 8:54 - Buku Lopatulika54 Yesu anayankha, Ngati Ine ndidzilemekeza ndekha, ulemerero wanga uli chabe; Atate wanga ndiye wondilemekeza Ine; amene munena za Iye, kuti ndiye Mulungu wanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Yesu anayankha, Ngati Ine ndidzilemekeza ndekha, ulemerero wanga uli chabe; Atate wanga ndiye wondilemekeza Ine; amene munena za Iye, kuti ndiye Mulungu wanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Yesu adati, “Ndikadzilemekeza ndekha, ulemu wangawo ngwachabe. Alipo ondilemekeza. Amenewo ndi Atate anga, omwe inuyo mumati ndi Mulungu wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Yesu anayankha kuti, “Ngati Ine ndidzilemekeza ndekha, ulemu wangawo ndi wosatanthauza kanthu. Atate anga amene inu mukuti ndi Mulungu wanu, ndiye amene amandilemekeza Ine. Onani mutuwo |