Yohane 8:53 - Buku Lopatulika53 Kodi Inu ndinu wamkulu ndi atate wathu Abrahamu, amene anamwalira? Ndipo aneneri anamwalira: mudziyesera nokha muli yani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Kodi Inu ndinu wamkulu ndi atate wathu Abrahamu, amene anamwalira? Ndipo aneneri anamwalira: mudziyesera nokha muli yani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Monga Iweyo nkupambana atate athu Abrahamu amene adamwalira? Anenerinso adamwalira. Kodi umadziyesa yani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Kodi ndinu wa mkulu kuposa abambo athu Abrahamu? Iye anafa, ndiponso aneneri onse. Inu mukuganiza kuti ndinu yani?” Onani mutuwo |