Yohane 8:3 - Buku Lopatulika3 Koma alembi ndi Afarisi anabwera naye kwa Iye mkazi wogwidwa m'chigololo, ndipo pamene anamuimika iye pakati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma alembi ndi Afarisi anabwera naye kwa Iye mkazi wogwidwa m'chigololo, ndipo pamene anamuimika iye pakati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Aphunzitsi a Malamulo pamodzi ndi Afarisi adabwera ndi mai amene adaamugwira akuchita chigololo, nkumukhalitsa pakati pao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Aphunzitsi amalamulo ndi Afarisi anabweretsa mkazi amene anagwidwa akuchita chigololo. Iwo anamuyimiritsa patsogolo pa anthu ndipo Onani mutuwo |