Yohane 8:2 - Buku Lopatulika2 Koma mamawa anadzanso ku Kachisi, ndipo anthu onse anadza kwa Iye; ndipo m'mene anakhala pansi anawaphunzitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma mamawa anadzanso ku Kachisi, ndipo anthu onse anadza kwa Iye; ndipo m'mene anakhala pansi anawaphunzitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 M'mamaŵa adabweranso ku Nyumba ya Mulungu. Anthu onse adadza kwa Iye, Iyeyo nkukhala pansi nayamba kuŵaphunzitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mmamawa Iye anaonekeranso ku Nyumba ya Mulungu kumene anthu onse anamuzungulira ndipo Iye anakhala pansi nawaphunzitsa. Onani mutuwo |