Yohane 8:22 - Buku Lopatulika22 Chifukwa chake Ayuda anenana, Kodi adzadzipha yekha, pakuti ananena, Kumene ndimukako Ine, simudziwa inu kudza? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chifukwa chake Ayuda anenana, Kodi adzadzipha yekha, pakuti ananena, Kumene ndimukako Ine, simudziwa inu kudza? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Apo Ayuda adati, “Kodi kapena akufuna kukadzipha, umo akunena kuti, ‘Kumene ndikupita Ine, inu simungathe kufikako?’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Izi zinachititsa Ayuda kufunsa kuti, “Kodi adzadzipha yekha? Kodi ndicho chifukwa chake akuti, ‘Kumene ndikupita, inu simungabwereko?’ ” Onani mutuwo |