Yohane 7:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti angakhale abale ake sanakhulupirire Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti angakhale abale ake sanakhulupirira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 (Ndiye kuti abale akewo ankatero chifukwa ngakhale iwo omwe sankamukhulupirira.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti ngakhale abale ake omwe sanamukhulupirire. Onani mutuwo |