Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 7:40 - Buku Lopatulika

40 Pamenepo ena a khamulo pakumva mau awa, ananena, Mneneriyo ndi uyu ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Pamenepo ena a khamulo pakumva mau awa, ananena, Mneneriyo ndi uyu ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Pamene khamu la anthu lidamva mau ameneŵa, ena mwa iwo ankati, “Zoonadi munthuyu ndiye Mneneri uja.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Pakumva mawu ake, ena a anthuwo anati, “Zoonadi munthu uyu ndi mneneri.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 7:40
6 Mawu Ofanana  

Ndipo makamu a anthu anati, Uyu ndi mneneri Yesu wa ku Nazarete wa ku Galileya.


Ndipo anamfunsa iye, Nanga bwanji? Ndiwe Eliya kodi? Nanena iye, Sindine iye. Ndiwe Mneneriyo kodi? Nayankha, Iai.


Mkazi ananena ndi Iye, Ambuye, ndizindikira kuti muli Mneneri.


Chifukwa chake, anthu, poona chizindikiro chimene anachita, ananena, kuti, Ameneyo ndiye mneneri ndithu wakudzayo m'dziko lapansi.


Ndipo kunali kung'ung'udza kwambiri za Iye m'makamu a anthu; ena ananena, kuti, Ali wabwino; koma ena ananena, Iai, koma asocheretsa khamu la anthuwo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa