Yohane 7:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo zitapita izi Yesu anayendayenda mu Galileya; pakuti sanafune kuyendayenda mu Yudeya, chifukwa Ayuda anafuna kumupha Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo zitapita izi Yesu anayendayenda m'Galileya; pakuti sanafune kuyendayenda m'Yudeya, chifukwa Ayuda anafuna kumupha Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Yesu ankayendera dera la Galileya. Sadafune kukayendera dera la Yudeya, chifukwa akuluakulu a Ayuda ankafuna kumupha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Zitatha izi Yesu anayendayenda mu Galileya, ndi cholinga chakuti asafike ku Yudeya chifukwa Ayuda kumeneko amadikira kuti amuphe. Onani mutuwo |