Yohane 6:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo iwo ananena, Si Yesu uyu, mwana wa Yosefe, atate wake ndi amai wake tiwadziwa? Anena bwanji tsopano, kuti, Ndinatsika Kumwamba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo iwo ananena, Si Yesu uyu, mwana wa Yosefe, atate wake ndi amai wake tiwadziwa? Anena bwanji tsopano, kuti, Ndinatsika Kumwamba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Iwo ankanena kuti, “Kodi ameneyu si Yesu, mwana wa Yosefe uja? Bambo wake ndi mai wake suja tikuŵadziŵa? Nanga tsono anganene bwanji kuti, ‘Ndidatsika kuchokera Kumwamba?’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Iwo anati, “Kodi uyu si Yesu, mwana wa Yosefe, amene abambo ake ndi amayi ake timawadziwa? Nanga Iyeyu akunena bwanji kuti, ‘Ine ndinatsika kuchokera kumwamba?’ ” Onani mutuwo |