Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 6:34 - Buku Lopatulika

34 Pamenepo anati kwa Iye, Ambuye, tipatseni ife mkate umene nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Pamenepo anati kwa Iye, Ambuye, tipatseni ife mkate umene nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Apo anthuwo adapempha Yesu kuti, “Ambuye, muzitipatsa chakudya chimenecho masiku onse.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Iwo anati, “Ambuye, kuyambira tsopano muzitipatsa buledi ameneyu.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 6:34
4 Mawu Ofanana  

Ambiri amati, Adzationetsa chabwino ndani? Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.


Mkaziyo ananena kwa Iye, Ambuye, ndipatseni madzi amene, kuti ndisamve ludzu, kapena ndisadze kuno kudzatunga.


Yesu anayankha iwo nati, Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Mundifuna Ine, si chifukwa munaona zizindikiro, koma chifukwa munadya mkate, nimunakhuta.


Mulungu Atate wa Ambuye Yesu, Iye amene alemekezeka kunthawi yonse, adziwa kuti sindinama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa