Yohane 6:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo pamene anampeza Iye tsidya lina la nyanja, anati kwa Iye, Rabi, munadza kuno liti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo pamene anampeza Iye tsidya lina la nyanja, anati kwa Iye, Rabi, munadza kuno liti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamene anthu aja adampeza Yesu kutsidya kwa nyanja, adamufunsa kuti, “Aphunzitsi, mudafika liti kuno?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Atamupeza mbali ina ya nyanjayo, iwo anamufunsa Iye kuti, “Rabi, mwafika nthawi yanji kuno?” Onani mutuwo |