Yohane 6:24 - Buku Lopatulika24 chifukwa chake pamene khamu la anthu linaona kuti palibe Yesu, ndi ophunzira ake palibe, iwo okha analowa m'ngalawazo nadza ku Kapernao, alikufuna Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 chifukwa chake pamene khamu la anthu linaona kuti palibe Yesu, ndi ophunzira ake palibe, iwo okha analowa m'ngalawazo nadza ku Kapernao, alikufuna Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Khamu lija lidaona kuti Yesu kulibe, ophunzira ake omwe kulibenso. Tsono anthu onsewo adaloŵa m'zombo zija, napita ku Kapernao kunka nafunafuna Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Nthawi yomwe gulu la anthu linaona kuti Yesu kapena ophunzira ake sanali pamenepo, ilo linalowanso mʼmabwatowo ndi kupita ku Kaperenawo kukamufunafuna Yesu. Onani mutuwo |