Yohane 6:23 - Buku Lopatulika23 koma zinachokera ngalawa zina ku Tiberiasi, pafupi pamalo pomwe adadyapo mkate m'mene Ambuye Yesu adayamika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 koma zinachokera ngalawa zina ku Tiberiasi, pafupi pa malo pomwe adadyapo mkate m'mene Ambuye Yesu adayamika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Komabe zombo zina zochokera ku Tiberiasi zidafika pafupi ndi malo amene anthu aja adaadyera chakudya Ambuye atayamika Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kenaka mabwato ena ochokera ku Tiberiya anafika pafupi ndi pamalo pamene anthu anadya buledi Ambuye atayamika. Onani mutuwo |