Yohane 6:21 - Buku Lopatulika21 Pamenepo analola kumlandira m'ngalawa; ndipo pomwepo ngalawayo inafika kumtunda kumene analikunkako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamenepo analola kumlandira m'ngalawa; ndipo pomwepo ngalawayo inafika kumtunda kumene analikunkako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Adamkweza Yesu m'chombomo mokondwa, ndipo nthaŵi yomweyo chombocho chidakocheza kumtunda kumene adaalingako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo iwo analola kumutenga mʼbwatomo, nthawi yomweyo bwatolo linafika ku gombe la nyanja kumene ankapita. Onani mutuwo |