Yohane 5:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo Ine sindilandira umboni kwa munthu: koma ndinena izi, kuti inu mukapulumutsidwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo Ine sindilandira umboni kwa munthu: koma ndinena izi, kuti inu mukapulumutsidwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Sikuti Ine ndikudalira umboni wa munthu, koma ndikunena izi kuti inu mupulumuke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Sikuti Ine ndikudalira umboni wa munthu; koma ndikunena zimenezi kuti mupulumutsidwe. Onani mutuwo |