Yohane 5:33 - Buku Lopatulika33 Inu munatuma kwa Yohane, ndipo iye anachitira umboni choonadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Inu munatuma kwa Yohane, ndipo iye anachitira umboni choonadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Inu nomwe mudaatuma amithenga anu kwa Yohane Mbatizi, ndipo iye adachitira umboni choona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Inu munatumiza amithenga kwa Yohane ndipo iye anachitira umboni choona. Onani mutuwo |