Yohane 5:31 - Buku Lopatulika31 Ngati ndichita umboni wa Ine ndekha, umboni wanga suli woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ngati ndichita umboni wa Ine ndekha, umboni wanga suli woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Ngati ndidzichitira ndekha umboni, umboni wangawo ngwosakwanira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Ngati ndidzichitira umboni ndekha, umboni wanga si woona. Onani mutuwo |