Yohane 5:26 - Buku Lopatulika26 Pakuti monga Atate ali ndi moyo mwa Iye yekha, momwemonso anapatsa kwa Mwana kukhala ndi moyo mwa Iye yekha; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pakuti monga Atate ali ndi moyo mwa Iye yekha, momwemonso anapatsa kwa Mwana kukhala ndi moyo mwa Iye yekha; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Monga Atate ali gwelo la moyo, momwemonso adaika Mwana wake kuti nayenso akhale gwelo la moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pakuti monga Atate ali gwero la moyo, momwemonso anapereka mphamvu zopereka moyo mwa Mwana. Onani mutuwo |