Yohane 4:7 - Buku Lopatulika7 Kunali ngati ora lachisanu ndi chimodzi. Kunadza mkazi wotuluka mu Samariya kudzatunga madzi. Yesu ananena naye, Undipatse Ine ndimwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Kunali ngati ora lachisanu ndi chimodzi. Kunadza mkazi wotuluka m'Samariya kudzatunga madzi. Yesu ananena naye, Undipatse Ine ndimwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono padafika mai wina wachisamariya kudzatunga madzi. Yesu nkunena mopempha kuti, “Zikomo mundipatseko madzi akumwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mayi wa Chisamariya atabwera kudzatunga madzi, Yesu anati kwa iye, “Kodi ungandipatse madzi akumwa.” Onani mutuwo |