Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 4:8 - Buku Lopatulika

8 Pakuti ophunzira ake adachoka kunka kumzinda kuti akagule chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Pakuti ophunzira ake adachoka kunka kumudzi kuti akagule chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nthaŵiyo nkuti ophunzira ake aja atakagula chakudya mu mzinda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 (Ophunzira ake nʼkuti atapita mʼmudzi kukagula chakudya).

Onani mutuwo Koperani




Yohane 4:8
7 Mawu Ofanana  

Koma anati kwa iwo, Muwapatse chakudya ndinu. Koma anati, Ife tilibe mikate, koma isanu yokha, ndi nsomba ziwiri zokha; kapena timuke ife kukagulira anthu awa onse zakudya.


Ndipo Yesu yemwe ndi ophunzira ake anaitanidwa kuukwatiwo.


Ndipo pamenepo anadza ophunzira ake; nazizwa kuti analinkulankhula ndi mkazi; koma panalibe wina anati, Mufuna chiyani? Kapena, mulankhula naye chiyani?


Ndipo m'mzinda muja anthu Asamariya ambiri anamkhulupirira Iye chifukwa cha mau a mkazi, wochita umboniyo, kuti, Anandiuza ine zinthu zilizonse ndinazichita.


Chifukwa chake anadza kumzinda wa Samariya, dzina lake Sikari, pafupi pa kadziko kamene Yakobo adapatsa mwana wake Yosefe;


Kunali ngati ora lachisanu ndi chimodzi. Kunadza mkazi wotuluka mu Samariya kudzatunga madzi. Yesu ananena naye, Undipatse Ine ndimwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa