Yohane 4:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo m'mene analikutsika, akapolo ake anakomana naye, nanena, kuti, Mwana wanu ali ndi moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo m'mene analikutsika, akapolo ake anakomana naye, nanena, kuti, Mwana wanu ali ndi moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Pa njira adakumana ndi antchito ake, ndipo iwo adamuuza kuti, “Mwana wanu wachira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Iye ali pa njira, antchito ake anakumana naye, namuwuza kuti mwana wanu uja wachira. Onani mutuwo |