Yohane 4:25 - Buku Lopatulika25 Mkazi ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti Mesiya adza (wotchedwa Khristu): akadzadza Iyeyu, adzatiuza zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Mkazi ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti Mesiya adza (wotchedwa Khristu): akadzadza Iyeyu, adzatiuza zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Maiyo adati, “Ndikudziŵa kuti akudza Mpulumutsi wolonjezedwa uja. Iyeyo akadzafika, adzatifotokozera zonse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mayiyo anati, “Ine ndikudziwa kuti Mesiya (wotchedwa Khristu) akubwera. Akabwera, Iye adzafotokoza zonse kwa ife.” Onani mutuwo |