Yohane 3:1 - Buku Lopatulika1 Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Munthu wina wa m'gulu la Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo panali Mfarisi wotchedwa Nekodimo, wa mʼgulu lolamulira la Ayuda. Onani mutuwo |