Yohane 21:4 - Buku Lopatulika4 Koma pakuyamba kucha, Yesu anaimirira pambali pa nyanja, komatu ophunzirawo sanadziwe kuti ndiye Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma pakuyamba kucha, Yesu anaimirira pambali pa nyanja, komatu ophunzirawo sanadziwa kuti ndiye Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kutacha Yesu adaimirira pa mtunda. Komabe ophunzira aja sadazindikire kuti ndi Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mmamawa, Yesu anayimirira mʼmbali mwa nyanja, koma ophunzira ake sanazindikire kuti anali Yesu. Onani mutuwo |