Yohane 21:2 - Buku Lopatulika2 Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wotchedwa Didimo, ndi Natanaele wa ku Kana wa ku Galileya, ndi ana a Zebedeo, ndi awiri ena a ophunzira ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wotchedwa Didimo, ndi Natanaele wa ku Kana wa ku Galileya, ndi ana a Zebedeo, ndi awiri ena a ophunzira ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Simoni Petro, Tomasi (wotchedwa Didimo), Natanaele wochokera ku mudzi wa Kana m'dera la Galileya, ana aja a Zebedeo, ndiponso ophunzira ena aŵiri, anali pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Simoni Petro, Tomasi (otchedwa Didimo), Natanieli wochokera ku Kana wa ku Galileya, ana a Zebedayo, ndi ophunzira ena awiri anali limodzi. Onani mutuwo |