Yohane 21:1 - Buku Lopatulika1 Zitapita izi Yesu anadzionetseranso kwa ophunzira ake kunyanja ya Tiberiasi. Koma anadzionetsera chotere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Zitapita izi Yesu anadzionetseranso kwa ophunzira ake kunyanja ya Tiberiasi. Koma anadzionetsera chotere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Yesu adadziwonetsanso kwa ophunzira ake ku nyanja ya Tiberiasi. Adadziwonetsa motere: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Zitatha izi Yesu anaonekeranso kwa ophunzira ake, mʼmbali mwa nyanja ya Tiberiya. Anadzionetsera motere: Onani mutuwo |