Yohane 20:16 - Buku Lopatulika16 Yesu ananena naye, Maria. Iyeyu m'mene anacheuka, ananena ndi Iye mu Chihebri, Raboni; chimene chinenedwa, Mphunzitsi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Yesu ananena naye, Maria. Iyeyu m'mene anacheuka, ananena ndi Iye m'Chihebri, Raboni; chimene chinenedwa, Mphunzitsi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Yesu adati, “Maria!” Iye adacheuka, nanena kuti, “Raboni!” (Ndiye kuti “Aphunzitsi” pa chihebri) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Yesu anati kwa iye, “Mariya.” Anatembenukira kwa Iye nafuwula mu Chiaramaiki kuti, “Raboni!” (kutanthauza Mphunzitsi). Onani mutuwo |