Yohane 2:12 - Buku Lopatulika12 Zitapita izi anatsikira ku Kapernao, Iye ndi amake, ndi abale ake, ndi ophunzira ake; nakhala komweko masiku owerengeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Zitapita izi anatsikira ku Kapernao, Iye ndi amake, ndi abale ake, ndi ophunzira ake; nakhala komweko masiku owerengeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake Yesu adapita ku Kapernao, pamodzi ndi amai ake ndi abale ake ndi ophunzira ake, ndipo adakhala kumeneko masiku oŵerengeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Zitatha izi Iye anatsikira ku Kaperenawo pamodzi ndi amayi ake, abale ake ndi ophunzira ake. Iwo anakhala kumeneko masiku owerengeka. Onani mutuwo |