Yohane 18:9 - Buku Lopatulika9 kuti akwaniridwe mau amene ati, Mwa iwo amene mwandipatsa Ine, sindinataye mmodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 kuti akwaniridwe mau amene ati, Mwa iwo amene mwandipatsa Ine, sindinataya mmodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 (Adaatero kuti zipherezere zimene Iye adaanena kale kuti, “Sindidatayepo ndi mmodzi yemwe mwa amene mudandipatsa.”) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Izi zinachitika kuti mawu amene Iye anayankhula akwaniritsidwe: “Ine sindinataye ndi mmodzi yemwe mwa iwo amene mwandipatsa.” Onani mutuwo |