Yohane 18:34 - Buku Lopatulika34 Yesu anayankha, Kodi munena ichi mwa inu nokha, kapena ena anakuuzani za Ine? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Yesu anayankha, Kodi munena ichi mwa inu nokha, kapena ena anakuuzani za Ine? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yesu adati, “Kodi mukunena zimenezi mwa inu nokha, kapena ena adakuuzani za Ine?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anafunsa kuti, “Kodi amenewo ndi maganizo anu wokha? Kapena kuti ena anakuwuzani za Ine?” Onani mutuwo |