Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 18:23 - Buku Lopatulika

23 Yesu anayankha iye, Ngati ndalankhula choipa, chita umboni wa choipacho, koma ngati bwino, undipandiranji?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Yesu anayankha iye, Ngati ndalankhula choipa, chita umboni wa choipacho, koma ngati bwino, undipandiranji?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Yesu adamuyankha kuti, “Ngati ndalankhula moipa, chitchule choipacho. Koma ngati ndalankhula moona, ukundimenyeranji?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Yesu anayankha kuti, “Ngati Ine ndanena kanthu kolakwika, chitirani umboni chimene ndalakwa. Koma ngati ndanena zoona, nʼchifukwa chiyani mwandimenya?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:23
4 Mawu Ofanana  

koma ndinena kwa inu, Musakanize munthu woipa; koma amene adzakupanda iwe pa tsaya lako lamanja, umtembenuzire linanso.


Koma ine ndekha Paulo, ndidandaulira inu mwa kufatsa ndi ulere wa Khristu, ine amene pamaso panu ndikhala wodzichepetsa pakati pa inu, koma pokhala kwina ine ndilimbika mtima kwa inu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa