Yohane 18:24 - Buku Lopatulika24 Koma Anasi adamtumiza Iye womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma Anasi adamtumiza Iye womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Anasi adatumiza Yesu ali chimangire kwa Kayafa, mkulu wa ansembe onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Kenaka Anasi anamutumiza Iye, ali womangidwabe, kwa Kayafa, mkulu wa ansembe. Onani mutuwo |