Yohane 18:2 - Buku Lopatulika2 Koma Yudasinso amene akampereka Iye, anadziwa malowa; chifukwa Yesu akankako kawirikawiri ndi ophunzira ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma Yudasinso amene akampereka Iye, anadziwa malowa; chifukwa Yesu akamkako kawirikawiri ndi ophunzira ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yudasi yemwe, amene adapereka Yesu kwa adani ake, ankaŵadziŵa malowo, pakuti Yesu ankapita kumeneko kaŵirikaŵiri ndi ophunzira ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsopano Yudasi, amene anamupereka amadziwa malowo chifukwa Yesu ankakumana ndi ophunzira ake kumeneko. Onani mutuwo |