Yohane 16:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo atadza Iyeyo, adzatsutsa dziko lapansi za machimo, ndi za chilungamo, ndi za chiweruziro; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo atadza Iyeyo, adzatsutsa dziko lapansi za machimo, ndi za chilungamo, ndi za chiweruziro; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo Iyeyu atafika, adzaŵatsimikiza anthu a pansi pano kuti ngolakwa pa za kuchimwa, za kulungama, ndiponso za kuweruza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye akabwera, adzatsutsa dziko lapansi za uchimo, zachilungamo ndi zachiweruzo. Onani mutuwo |