Yohane 16:6 - Buku Lopatulika6 Koma chifukwa ndalankhula izi ndi inu chisoni chadzala mumtima mwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma chifukwa ndalankhula izi ndi inu chisoni chadzala mumtima mwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 M'mitima mwanu mwadzaza chisoni chifukwa ndakuuzani zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Muli ndi chisoni kwambiri chifukwa ndakuwuzani zimene. Onani mutuwo |