Yohane 16:18 - Buku Lopatulika18 Chifukwa chake ananena. Ichi nchiyani chimene anena, Kanthawi? Sitidziwa chimene alankhula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Chifukwa chake ananena. Ichi nchiyani chimene anena, Kanthawi? Sitidziwa chimene alankhula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Kodi nchiyani akunenachi kuti, ‘Kanthaŵi pang'ono?’ Sitikumvetsa zimene akufuna kunena.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo anapitiriza kufunsana kuti, “Kodi akutanthauza chiyani, ‘kanthawi kochepa?’ Ife sitikumvetsetsa chimene Iye akuyankhula.” Onani mutuwo |