Yohane 16:1 - Buku Lopatulika1 Izi ndalankhula ndi inu kuti mungakhumudwitsidwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Izi ndalankhula ndi inu kuti mungakhumudwitsidwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 “Ndakuuziranitu zonsezi kuti mungadzataye mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 “Ine ndakuwuzani zonsezi kuti musadzakhumudwe. Onani mutuwo |