Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 14:8 - Buku Lopatulika

8 Filipo ananena ndi Iye, Ambuye, tionetsereni ife Atate, ndipo chitikwanira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Filipo ananena ndi Iye, Ambuye, tionetsereni ife Atate, ndipo chitikwanira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Filipo adati, “Ambuye, tiwonetseni Atatewo, mukatero tikhutira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Filipo anati, “Ambuye, tionetseni Atatewo ndipo ife tikhutitsidwa.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 14:8
12 Mawu Ofanana  

Apembedza Mulungu, ndipo amkomera mtima; m'mwemo aona nkhope yake mokondwera; ndipo ambwezera munthu chilungamo chake.


Koma ine ndidzapenyerera nkhope yanu m'chilungamo, ndidzakhuta mtima ndi maonekedwe anu, pamene ndidzauka.


Kuti ndione mphamvu yanu ndi ulemerero wanu, monga ndinakuonani m'malo oyera.


Odala ali oyera mtima; chifukwa adzaona Mulungu.


Natanaele ananena naye, Munandidziwira kuti? Yesu anayankha nati kwa iye, Asanakuitane Filipo, pokhala iwe pansi pa mkuyu paja, ndinakuona iwe.


Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa