Yohane 14:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo kumene ndinkako Ine, mudziwa njira yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo kumene ndinkako Ine, mudziwa njira yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndipo kumene ndikupita Ineko, njira yake mukuidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Inu mukudziwa njira ya kumene Ine ndikupita.” Onani mutuwo |