Yohane 14:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Ine ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani inu Nkhoswe ina, kuti akhale ndi inu kunthawi yonse, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Ine ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani inu Nkhoswe ina, kuti akhale ndi inu kunthawi yonse, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pamenepo ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani Nkhoswe ina kuti izikhala nanu nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ine ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani Nkhoswe ina kuti izikhala nanu nthawi zonse. Onani mutuwo |