Yohane 13:4 - Buku Lopatulika4 ananyamuka pamgonero, navula malaya ake; ndipo m'mene adatenga chopukutira, anadzimanga m'chuuno. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ananyamuka pamgonero, navula malaya ake; ndipo m'mene adatenga chopukutira, anadzimanga m'chuuno. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho pamene analikudya, Yesu adaimirira, adavula mwinjiro wake, natenga nsalu yopukutira nkuimanga m'chiwuno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 anayimirira kuchoka pa chakudya navula zovala zake natenga nsalu yopukutira nadzimanga mʼchiwuno mwake. Onani mutuwo |