Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 13:30 - Buku Lopatulika

30 Pamenepo iyeyo m'mene adalandira nthongo, anatuluka pomwepo. Koma kunali usiku.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Pamenepo iyeyo m'mene adalandira nthongo, anatuluka pomwepo. Koma kunali usiku.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Yudasi atalandira mkate uja, pompo adatuluka. Nthaŵiyo nkuti kutada kale.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Nthawi yomweyo Yudasi atangodya buledi, anatuluka, ndipo unali usiku.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 13:30
6 Mawu Ofanana  

Pakuti akapanda kuchita zoipa, samagona; ndipo akapanda kukhumudwitsa wina, tulo tao tiwachokera.


Mapazi ao athamangira koipa, ndipo iwo afulumira kukhetsa mwazi wosachimwa; maganizo ao ali maganizo oipa; bwinja ndi chipasuko zili m'njira mwao.


Masiku onse, pamene ndinali ndi inu mu Kachisi, simunatanse manja anu kundigwira: koma nyengo ino ndi yanu, ndipo ulamuliro wa mdima ndi wanu.


Ndipo Yesu anayankha, Ndi iyeyu, amene Ine ndidzamsunsira nthongo ndi kumpatsa. Pamenepo, m'mene anasunsa nthongo anaitenga naipatsa Yudasi mwana wa Simoni Iskariote.


miyendo yao ichita liwiro kukhetsa mwazi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa