Yohane 13:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti anadziwa amene adzampereka Iye; chifukwa cha ichi anati, Simuli oyera nonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti anadziwa amene adzampereka Iye; chifukwa cha ichi anati, Simuli oyera nonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Yesu ankamudziŵa munthu wodzampereka kwa adani ake, nchifukwa chake adaati, “Si nonsenu muli oyera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pakuti Iye anadziwa amene adzamupereka, ndipo nʼchifukwa chake anati saliyense wa inu ali woyera. Onani mutuwo |