Yohane 12:4 - Buku Lopatulika4 Koma Yudasi Iskariote, mmodzi wa ophunzira ake, amene adzampereka Iye, ananena, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma Yudasi Iskariote, mmodzi wa ophunzira ake, amene adzampereka Iye, ananena, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma Yudasi Iskariote, mmodzi mwa ophunzira a Yesu, amene analikudzampereka kwa adani ake, adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma mmodzi wa ophunzira ake, Yudasi Isikarioti, amene pambuyo pake adzamupereka anati, Onani mutuwo |